Ama 2 sauzande akupwetekani aMolotoni -Wikise
Oyimba wamdziko muno Wikise yemwe dzina lake lenileni ndi Frank Chawinga watulutsa nyimbo yoonera m'mawa lero ‘aMolo’ yomwe akulangiza abambo...